Isaiah 65:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma inu amene mumakana Chauta, amene mumaiŵala phiri langa lopatulika, amene mumapembedza Gadi ndi Meni, milungu yobweretsa mwai ndi tsoka,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma inu amene mwasiya Yehova, amene mwaiwala phiri langa lopatulika, ndi kukonzera mulungu wamwai gome, ndi kudzazira mulungu waimfa zikho za vinyo wosanganiza;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Koma inu amene mumasiya Yehova ndi kuyiwala phiri langa lopatulika, amene munamukonzera Gadi chakudya ndi kuthirira Meni chakumwa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma inu amene mwasiya Yehova, amene mwaiwala phiri langa lopatulika, ndi kukonzera mlungu wamwai gome, ndi kudzazira mlungu waimfa zikho za vinyo wosanganiza;