Isaiah 66:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakusangalatsani ku Yerusalemu monga momwe mai amasangalatsira mwana wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Monga munthu amene amake amtonthoza mtima, momwemo ndidzatonthoza mtima wanu; ndipo mudzatonthozedwa mtima m'Yerusalemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Monga momwe amayi amasangalatsira mwana wawo, moteronso Ine ndidzakusangalatsani; ndipo mudzasangalala chifukwa cha Yerusalemu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Monga munthu amene amace amtonthoza mtima, momwemo ndidzatonthoza mtima wanu; ndipo mudzatonthozedwa mtima m'Yerusalemu.