Isaiah 66:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mzinda wangawu uli ngati mai amene akubadwitsa mwana asanayambe kumva zoŵaŵa zake, amene akubala mwana wamwamuna kupweteka kusanayambike.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mkazi asanamve zowawa, anabala mwana; kupweteka kwake kusanadze, anabala mwana wamwamuna.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Mzinda uli ngati amayi apakati amene asanayambe kumva zowawa wachira kale; asanayambe kumva ululu, wabala kale mwana wamwamuna.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mkazi asanamve zowawa, anabala mwana; kupweteka kwace kusanadze, anabala mwana wamwamuna.