Isaiah 8:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adandilangiza mwamphamvu, ndipo adandichenjeza kuti ndisamayenda m'njira ya anthuŵa. Adati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti Yehova watero kwa ine ndi dzanja lolimba, nandilangiza ine kuti ndisayende m'njira ya anthu awa, nati,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anandiyankhula ine mwamphamvu, ndipo anandichenjeza kuti ndisamayende mʼnjira za anthuwa. Iye anati:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti Yehova watero kwa ine ndi dzanja lolimba, nandilangiza ine kuti ndisayende m'njira ya anthu awa, nati,