Isaiah 8:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Manga bwino umboniwu ndipo umatepo chimatiro pa mau ameneŵa, pamaso pa ophunzira anga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Manga umboni, mata chizindikiro pachilamulo mwa aphunzi anga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Manga umboniwu ndipo umate malamulowa pamaso pa ophunzira anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Manga umboni, mata cizindikilo pacilamulo mwa aphunzi anga.