Isaiah 8:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Onani, ine ndi ana amene Chauta wandipatsa, ndife zizindikiro ndi zidziŵitso kwa Aisraele zofuma kwa Chauta Wamphamvuzonse amene amakhala pa phiri la Ziyoni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa ine, tili zizindikiro ndi zodabwitsa mwa Israele, kuchokera kwa Yehova wa makamu, amene akhala m'phiri la Ziyoni.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Onani, ine ndili pano pamodzi ndi ana amene Yehova wandipatsa, ndife zizindikiro ndi zodabwitsa kwa Aisraeli zochokera kwa Yehova Wamphamvuzonse, amene amakhala pa Phiri la Ziyoni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa ine, tiri zizindikilo ndi zodabwitsa mwa Israyeli, kucokera kwa Yehova wa makamu, amene akhala m'phiri la Ziyoni.