Isaiah 8:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu adzayendayenda m'dziko movutika kwambiri ali ndi njala. Chifukwa cha njalayo, adzakalipa, ndipo adzayang'ana kumwamba ndi kutemberera mfumu yao ndi Mulungu wao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwo adzapitirira ovutidwa ndi anjala, ndipo padzakhala kuti pokhala ndi njala iwo adzadziputa okha, ndi kutemberera mfumu yao, ndi Mulungu wao; ndi kugadamira nkhope zao kumwamba;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu adzayendayenda mʼdziko movutika kwambiri ali ndi njala; pamene afowokeratu ndi njala, iwo adzakwiya kwambiri ndipo adzayangʼana kumwamba ndi kutemberera mfumu yawo ndi Mulungu wawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwo adzapitirira obvutidwa ndi anjala, ndipo padzakhala kuti pokhala ndi njala iwo adzadziputa okha, ndi kutemberera mfumu yao, ndi Mulungu wao; ndi kugadamira nkhope zao kumwamba;