Isaiah 8:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma akadzayang'ana pa dziko, adzangoona mavuto okhaokha ndi mdima woopsa ndi wodetsa nkhaŵa. Adzaponyedwa mu mdima wandiweyani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nadzayang'ana padziko, koma taonani, nkhawa ndi mdima, kuziya kwa nsautso; ndi mdima woti bii udzaingitsidwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo akadzayangʼana pa dziko lapansi adzangoona mavuto okhaokha ndi mdima woopsa ndi wodetsa nkhawa, ndipo adzaponyedwa mu mdima wandiweyani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nadzayang'ana padziko, koma taonani, nkhawa ndi mdima, kuziya kwa nsautso; ndi mdima woti bi udzaingitsidwa.