Isaiah 8:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Patapita nthaŵi mkazi wanga adaima, nabala mwana wamwamuna. Pamenepo Chauta adandiwuza kuti, “Umutche dzina lakuti KUSAKAZA-KWAMSANGA-KUFUNKHA-KOFULUMIRA.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndinanka kwa mneneri wamkazi; ndipo iye anatenga pakati nabala mwana wamwamuna. Ndipo Yehova anati kwa ine, Utche dzina lake, Kangazakufunkha Fulumirakusakaza.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo ine ndinapita kwa mneneri wamkazi, ndipo anakhala woyembekezera nabala mwana wamwamuna. Ndipo Yehova anati kwa ine, “Umutche dzina lakuti, ‘Kusakaza-Kwamsanga Kufunkha-Kofulumira.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndinanka kwa mneneri wamkazi; ndipo iye anatenga pakati nabala mwana wamwamuna. Ndipo Yehova anati kwa ine, Uche dzina lace, Kangazakufunkha Fulumirakusakaza.