Isaiah 8:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Anthu a dziko ili akana madzi anga a ku Siloamu oyenda mwachifatse, ndipo amakondwerera Rezini ndi mwana wa Remaliya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Popeza anthu awa akana madzi a Siloamu, amene ayenda pang'onopang'ono, nakondwerera mwa Rezini ndi mwa mwana wa Remaliya;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Popeza anthu a dziko ili akana madzi anga oyenda mwachifatse a ku Siloamu, ndipo akukondwerera Rezini ndi mwana wa Remaliya,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Popeza anthu awa akana madzi a Silowa, amene ayenda pang'ono pang'ono, nakondwerera mwa Rezini ndi mwa mwana wa Remaliya;