Isaiah 9:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Chauta waŵautsira adani, Waŵakhwirizira adaniwo kuti amenyane nawo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake Yehova adzamkwezera Rezini olimbana naye, nautsa adani ake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yehova wadzutsa adani kuti alimbane nawo ndipo wawafulumiza adani awo kuti amenyane nawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace Yehova adzamkwezera Rezini olimbana naye, nautsa adani ace;