Isaiah 9:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake Chauta wadula mutu wa Israele pamodzi ndi mchira womwe, nthambi ya kanjedza ndi bango lomwe pa tsiku limodzi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake Yehova adzadula mutu wa Israele ndi mchira wake; nthambi ya kanjedza ndi mlulu, tsiku limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Yehova adzadula mutu wa Israeli pamodzi ndi mchira womwe, nthambi ya kanjedza ndi bango lomwe tsiku limodzi;
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace Yehova adzadula mutu wa Israyeli ndi mcira wace; nthambi ya kanjedza ndi mlulu, tsiku limodzi.