Isaiah 9:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ku dzanja lamanja amapeza ndi kudya chakudya, koma osakhuta, ku dzanja lamanzere amapeza ndi kudya chakudya, koma njala ali nayobe. Kwatsala nkumangodyana okhaokha.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo wina adzakwatula ndi dzanja lamanja, nakhala ndi njala; ndipo adzadya ndi dzanja lamanzere, osakhutai; iwo adzadya munthu yense nyama ya mkono wake wa iye mwini.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kudzanja lamanja adzapeza chakudya nʼkudya, koma adzakhalabe ndi njala; kudzanja lamanzere adzapeza chakudya nʼkudya, koma sadzakhuta. Aliyense azidzadya ana ake omwe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo wina adzakwatula ndi dzanja lamanja, nakhala ndi njala; ndipo adzadya ndi dzanja lamanzere, osakhutai; iwo adzadya munthu yense nyama ya mkono wace wa iye mwini.