James 1:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Abale anga, muzikondwa ndithu mukamayesedwa ndi mavuto amitundumitundu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muchiyese chimwemwe chokha, abale anga, m'mene mukugwa m'mayesero a mitundumitundu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abale, muchiyese ngati chimwemwe chenicheni nthawi zonse pamene mukukumana ndi mayesero amitundumitundu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muciyese cimwemwe cokha, abale anga, m'mene mukugwa m'mayesero a mitundu mitundu;