James 1:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Paja munthu wokwiya safikapo pa chilungamo chimene amafuna Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti mkwiyo wa munthu suchita chilungamo cha Mulungu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pakuti mkwiyo wa munthu subweretsa chilungamo chimene amafuna Mulungu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti mkwiyo wa munthu sucita cilungamo ca Mulungu.