James 1:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono amati akadzipenya, amachokapo, posachedwa nkuiŵalako m'mene akuwonekera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pakuti wadziyang'anira yekha, nachoka, naiwala pompaja nali wotani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Akadziyangʼana amachoka, nthawi yomweyo nʼkuyiwala mmene akuonekera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pakuti wadziyang'anira yekha nacoka, naiwala pompaja nali wotani.