James 1:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
pakuti iyeyo ndi wa mitima iŵiri, ndi wosakhazikika pa zochita zake zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
munthu wa mitima iwiri akhala wosinkhasinkha pa njira zake zonse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iyeyu ndi munthu wa mitima iwiri, wosakhazikika pa zimene akuchita.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
munthu wa mitima iwiri akhala wosinkhasinkha pa njira zace zonse.