James 1:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mbale woluluka anyadire pamene Mulungu amkweza.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma mbale woluluka adzitamandire pa ukulu wake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abale omwe ndi anthu wamba anyadire pamene akwezedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma mbale woluluka adzitamandire pa ukulu wace;