James 2:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwachitsanzo: mbale wina kapena mlongo ali ndi usiŵa, ndipo masiku onse alibe chakudya chokwanira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mbale kapena mlongo akakhala wausiwa, nichikamsowa chakudya cha tsiku lake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tangoganizirani, mʼbale kapena mlongo amene ali ndi usiwa, ndipo alibe chakudya cha tsiku ndi tsiku.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mbale kapena mlongo akakbalawausiwa, nieikamsowa cakudya ca tsiku lace,