James 2:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nanga Abrahamu, kholo lathu, suja adakhala wolungama pamaso pa Mulungu chifukwa cha ntchito yomwe adachita, muja adaapereka mwana wake Isaki pa guwa lansembe?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Abrahamu kholo lathu, sanayesedwa wolungama ndi ntchito kodi, paja adapereka mwana wake Isaki nsembe pa guwa la nsembe?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi Abrahamu kholo lathu sanatengedwe kukhala wolungama chifukwa cha zimene anachita pamene anapereka mwana wake Isake pa guwa lansembe?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Abrabamu kholo lathu, sanayesedwa wolungama ndi nchito kodi, paja adapereka mwana wace Isake nsembe pa guwa la nsembe?