James 2:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi suja zidaateronso ndi Rahabu, mkazi wadama uja? Iye adaalandira azondi aja, nkuŵabweza kwao poŵadzeretsa njira ina, ndipo adapezeka kuti ngwolungama pamaso pa Mulungu chifukwa cha zimene adaachitazo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo momwemonso sanayesedwa wolungama Rahabu mkazi wa damayo ndi ntchito kodi, popeza adalandira amithenga, nawatulutsa adzere njira ina?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nʼchimodzimodzinso, kodi wadama uja, Rahabe, sanasanduke wolungama chifukwa cha zomwe anachita pamene anapereka malo ogona kwa azondi aja ndi kuwathawitsira mbali ina?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo momwemonso sanayesedwa wolungama Rahabi mkazi wa damayo ndi nchito kodi, popeza adalandira amithenga, nawaturutsa adzere njira yina?