James 2:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma mukamaonetsa kukondera, mukuchimwa, ndipo Malamulo a Mulungu akukutsutsani kuti ndinu opalamula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma ngati musamala maonekedwe, muchita uchimo, ndipo mutsutsidwa ndi chilamulo monga olakwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mukamaonetsa tsankho mukuchimwa, ndipo ndinu wochimwa monga wophwanya lamulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma ngati musamala maonekedwe, mucita ucimo, ndipo mutsutsidwa ndi cilamulo monga olakwa.