James 4:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma monga zilirimu, mumanyada ndi kudzitama. Kunyada konse kotere nkoipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma tsopano mudzitamandira m'kudzikuza kwanu; kudzitamandira kulikonse kotero nkoipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma mmene zililimu mumangodzitama ndi kudzikuza. Kudzitama konse kotereku ndi koyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma tsopano mudzitamandira m'kudzikuza kwanu; kudzitamandira kuli konse kotero nkoipa.