James 5:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mverani tsono, inu anthu achumanu. Lirani ndi kufuula chifukwa cha zovuta zimene zikudzakugwerani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nanga tsono achuma inu, lirani ndi kuchema chifukwa cha masautso anu akudza pa inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono tamverani, inu anthu achuma, lirani ndi kufuwula chifukwa cha zovuta zimene zidzakugwereni.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nanga tsono acuma inu, lirani ndi kucema cifukwa ca masautso anu akudza pa inu,