James 5:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi wina mwa inu ali m'mavuto? Apemphere. Kodi wina wakondwa? Aimbe nyimbo zotamanda Mulungu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi wina wa inu akumva zowawa? Apemphere. Kodi wina asekera? Aimbire.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi alipo wina mwa inu amene ali pa mavuto? Apemphere. Kodi wina wakondwa? Ayimbe nyimbo zolemekeza.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi wina wa inu akumva zowawa? Apemphere, Kodi wina asekera? Ayimbire.