Jeremiah 11:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adandiwululira, ndipo ndidadziŵa za chiwembu cha anthu. Iye adatsekula maso anga nandiwonetsa ntchito zao zoipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yehova anandidziwitsa, ndipo ndinadziwa; ndipo wandisonyeza ine machitidwe ao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anandiwululira ndipo ndinadziwa. Iye anatsekula maso anga kuti ndione chiwembu chawocho.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yehova anandidziwitsa, ndipo ndinadziwa; ndipo wandisonyeza ine macitidwe ao.