Jeremiah 11:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake Chauta Wamphamvuzonse akunena kuti, “Ndidzaŵalanga. Anyamata ao adzaphedwa ku nkhondo. Ana ao aamuna ndi aakazi adzafa ndi njala.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
chifukwa chake atero Yehova wa makamu, Taonani, ndidzalanga iwo; anyamata adzafa ndi lupanga; ana ao aamuna ndi aakazi adzafa ndi njala;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
koma Yehova Wamphamvuzonse akuti, ‘Ine ndidzawalanga. Achinyamata awo adzaphedwa ndi lupanga, ana awo aamuna ndi aakazi adzafa ndi njala.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
cifukwa cace atero Yehova wa makamu, Taonani, ndidzalanga iwo; anyamata adzafa ndi lupanga; ana ao amuna ndi akazi adzafa ndi njala;