Jeremiah 11:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sadzapulumuka ndi mmodzi yemwe, chifukwa ndidzaononga anthu a ku Anatoti, chikadzafika chaka chao cha chilango.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo sadzakhala nao otsalira; pakuti ndidzatengera choipa pa anthu a ku Anatoti, chaka cha kulangidwa kwao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sipadzakhala otsala ndi mmodzi yemwe, chifukwa ndidzalanga anthu a ku Anatoti chikadzafika chaka chawo cha chilango.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo sadzakhala nao otsalira; pakuti ndidzatengera coipa pa anthu a ku Anatoti, caka ca kulangidwa kwao.