Jeremiah 11:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Uŵauze kuti mau a Chauta, Mulungu wa Israele, ndi aŵa: Atembereredwe munthu amene sasunga mau a chipangano,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi kunena kwa iwo, Atero Yehova, Mulungu wa Aisraele: Wotembereredwa ndi munthu wosamvera mau a pangano ili,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Awuze kuti Yehova, Mulungu wa Israeli akuti ‘adzakhala wotembereredwa munthu amene samvera mawu a pangano ili.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi kunena kwa iwo, Atero Yehova, Mulungu wa Aisrayeli: Wotembereredwa ndi munthu wosamvera mau a pangano ili,