Jeremiah 12:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Komabe nditaŵachotsa, ndidzaŵamveranso chifundo, ndipo ndidzabwezanso mtundu uliwonse ku dziko la choloŵa chake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo padzakhala kuti nditazula iwo, ndidzabwera, ndipo ndidzawachitira chisoni; ndipo ndidzabwezanso iwo, yense ku cholowa chake, ndi yense kudziko lake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe nditawachotsa, ndidzawachitiranso chifundo, ndipo ndidzabwezera aliyense cholowa chake ndi dziko lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo padzakhala kuti nditazula iwo, ndidzabwera, ndipo ndidzawacitira cisoni; ndipo ndidzabwezanso iwo, yense ku colowa cace, ndi yense ku dziko lace.