Jeremiah 12:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Inu mudaŵabzala, ndipo adamera mizu. Amakula, namabala zipatso. Amakonda kulankhula za Inu, koma mitima yao ili kutali ndi Inu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Inu Mwabzala iwo, inde, anagwiritsatu mizu; amera, inde, abalatu zipatso; muli pafupi m'kamwa mwao, muli patali ndi impso zao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Inu munawadzala ndipo anamera mizu; amakula ndi kubereka zipatso. Dzina lanu limakhala pakamwa pawo nthawi zonse, koma mitima yawo imakhala kutali ndi Inu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Inu mwabzyala iwo, inde, anagwiritsatu mizu; amera, inde, abalatu zipatso; muli pafupi m'kamwa mwao, muli patari ndi imso zao.