Jeremiah 13:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi munthu wakuda nkusintha khungu lake? Kodi kambuku nkusintha maŵanga ake? Ndiye kuti inuyo, ozoloŵera kuchimwanu, mungathe kumachita zabwino ngati?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi angathe Mkusi kusanduliza khungu lake, kapena nyalugwe mawanga ake? Pamenepo mungathe inunso kuchita zabwino, inu amene muzolowera kuchita zoipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi wa dziko la Kusi nʼkusintha khungu lake, kapena kambuku kusintha mawanga ake? Inunso amene munazolowera kuchita zoyipa simungathe kusintha.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi angathe Mkusi kusanduliza khungu lace, kapena nyalugwe maanga ace? pamenepo mungathe inunso kucita zabwino, inu amene muzolowera kucita zoipa,