Jeremiah 13:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa cha kuipa kwanuko, ndidzakumwazani ngati mankhusu, onka nauluka ndi mphepo yakuchipululu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake ndidzabalalitsa iwo, monga ziputu zakupita, ndi mphepo ya kuchipululu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Ine ndidzakumwazani ngati mankhusu amene amawuluka ndi mphepo ya ku chipululu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace ndidzabalalitsa iwo, monga ziputu zakupita, ndi mphepo ya kucipululu.