Jeremiah 13:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adandiwuzanso mau kachiŵiri kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mau a Yehova anadza kwa ine nthawi yachiwiri, kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka Yehova anandiyankhulanso kachiwiri kuti,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mau a Yehova anadza kwa ine nthawi yaciwiri, kuti,