Jeremiah 15:11 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta adayankha kuti, “Koma zoonadi ndidzakulanditsa kuti upeze bwino. Ndithudi, adani ako adzakupemba pa nthaŵi ya tsoka ndi ya mavuto.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Yehova anati, Ndithu ndidzakulimbitsira iwe zabwino; ndithu ndidzapembedzetsa mdani kwa iwe nthawi ya zoipa ndi nthawi ya nsautso.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova anati, “Ndithudi, Ine ndidzakulanditsa kuti upeze bwino. Ndithudi, adani ako adzakupempha pa nthawi ya tsoka ndi ya mavuto awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Yehova anati, Ndithu ndidzakulimbitsira iwe zabwino; ndithu ndidzapembedzetsa mdani kwa iwe nthawi ya zoipa ndi nthawi yansautso.