Jeremiah 15:13 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Anthu inu, chuma chanu chonse pamodzi ndi katundu wanu ndidzazipereka kwa ofunkha popanda malipiro, chifukwa cha machimo anu ambiri m'dziko lonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chuma chako ndi zosungidwa zako ndidzazipereka zifunkhidwe kopanda mtengo wake, ichicho chidzakugwera chifukwa cha zochimwa zako zonse, m'malire ako onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu ako ndi chuma chako ndidzazipereka kwa ofunkha popanda malipiro, chifukwa cha machimo anu onse a mʼdziko lanu lonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cuma cako ndi zosungidwa zako ndidzazipereka zifunkhidwe kopanda mtengo wace, icico cidzakugwera cifukwa ca zocimwa zako zonse, m'malire ako onse.