Jeremiah 15:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzakusandutsani akapolo a adani anu m'dziko limene simulidziŵa. Ndithudi, mkwiyo wanga wayaka, ndipo udzakutenthani kosalekeza.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzawapititsa iwo pamodzi ndi adani ako kudziko limene sudziwa iwe; pakuti moto wayaka m'mkwiyo wanga, umene udzatentha inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzakusandutsani akapolo a adani anu mʼdziko limene inu simulidziwa, chifukwa mkwiyo wanga wayaka ngati moto umene udzakutenthani.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzawapititsa iwo pamodzi ndi adani ako ku dziko limene sudziwa iwe; pakuti moto wayaka m'mkwiyo wanga, umene udzatentha inu.