Jeremiah 15:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Sindidakhale nao m'gulu la anthu amadyera, sindidasangalale nawo anthu amenewo. Ndidakhala ndekha chifukwa choti dzanja lanu linali pa ine, ndipo mumtima mwanga mudadzaza mkwiyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Sindinakhala m'msonkhano wa iwo amene asekerasekera, ndi kusangalala; ndinakhala pandekha chifukwa cha dzanja lanu; pakuti mwandidzaza ndi mkwiyo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Sindinakhale nawo mʼgulu la anthu amadyera, sindinasangalale nawo anthu amenewo. Ndinakhala ndekha chifukwa choti dzanja lanu linali pa ine ndipo munadzaza mu mtima mwanga ndi mkwiyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Sindinakhala m'msonkhano wa iwo amene asekera-sekera, ndi kusangalala; ndinakhala pandekha cifukwa ca dzanja lanu; pakuti mwandidzaza ndi mkwiyo.