Jeremiah 15:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzaŵasandutsa chinthu chochititsa nyansi kwa anthu a m'maufumu onse a dziko lapansi, chifukwa cha zimene Manase mwana wa Hezekiya, mfumu ya ku Yuda, adachita ku Yerusalemu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo ndidzawapereka akhale oopsetsa m'maufumu onse a dziko lapansi, chifukwa cha Manase mwana wa Hezekiya mfumu ya Yuda, chifukwa cha zija anachita m'Yerusalemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndidzawasandutsa kukhala chinthu chonyansa kwa anthu a maufumu onse a dziko lapansi chifukwa cha zimene Manase mwana wa Hezekiya mfumu ya Yuda anachita mu Yerusalemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo ndidzawapereka akhale oopsetsa m'maufumu onse a dziko lapansi, cifukwa ca Manase mwana wa Hezekiya mfumu ya Yuda, cifukwa ca zija anacita m'Yerusalemu.