Jeremiah 15:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akuti, “Kodi inu a ku Yerusalemu adzakumverani chisoni ndani? Adzakulirani ndani? Ndani adzapatuke kuti akufunseni za moyo wanu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakuti ndani adzakuchitira iwe chisoni, Yerusalemu? Ndani adzakulirira iwe? Ndani adzapatukira kudzafunsa za mkhalidwe wako?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Kodi adzakumvera chisoni ndani, Yerusalemu? Kodi adzakulira ndani? Kodi ndani amene adzapatuka kufunsa za moyo wako?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakuti ndani adzakucitira iwe cisoni, Yerusalemu? ndani adzakulirira iwe? ndani adzapatukira kudzafunsa za mkhalidwe wako?