Jeremiah 17:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chauta akuti, “Uchimo wa Yuda ndi wolembedwa ndi cholembera chachitsulo, cha nsonga ya mwala wadaimondi. Uchimowo walembedwa pa mitima yao ndiponso pa maguwa ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tchimo la Yuda lalembedwa ndi peni lachitsulo, ndi nsonga ya diamondi; lalembedwa pa cholembapo cha m'mtima mwao, ndi pa nyanga za maguwa a nsembe anu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tchimo la Yuda lazokotedwa ndi cholembera cha chitsulo, lalembedwa ndi msonga ya mwala wadayimondi. Uchimowo walembedwa pa mitima yawo ndiponso pa nyanga za maguwa awo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cimo la Yuda lalembedwa ndi peni lacitsulo, ndi nsonga ya diamondi; lalembedwa pa colembapo ca m'mtima mwao, ndi pa nyanga za maguwa a nsembe anu.