Jeremiah 17:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu akundifunsa kuti, “Zija ankanena Chautazi zili kuti? Zitachitikatu kuti tiziwone!”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, ati kwa ine, Mau a Yehova ali kuti? Adze tsopano.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthu akumandinena kuti, “Mawu a Yehova ali kuti? Zichitiketu lero kuti tizione!”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, ati kwa ine, Mau a Yehova ali kuti? adze tsopano.