Jeremiah 17:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ukanene kuti: Imvani mau a Chauta, inu mafumu a ku Yuda, inu anthu a ku Yuda, ndi inu nonse okhala mu Yerusalemu amene mumaloŵera pa zipata zimenezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo uziti kwa iwo, Tamvani mau a Yehova, inu mafumu a Yuda, ndi Ayuda onse, ndi onse okhala m'Yerusalemu, amene alowa pa zipatazi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ukawawuze kuti, ‘Imvani mawu a Yehova, inu mafumu onse a ku Yuda ndi anthu onse a ku Yuda ndi inu nonse okhala mu Yerusalemu amene mumatulukira pa zipata izi.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo uziti kwa iwo, Tamvani mau a Yehova, inu mafumu a Yuda, ndi Ayuda onse, ndi onse okhala m'Yerusalemu, amene alowa pa zipatazi;