Jeremiah 17:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
M'mau a Chautawo ndi aŵa: Kuti musunge moyo wanu, samalani bwino kuti pa tsiku la Sabata musanyamule katundu, kapena kuloŵa naye pa zipata za Yerusalemu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
atero Yehova: Tadzayang'anirani nokha, musanyamule katundu tsiku la Sabata, musalowe naye pa zipata za Yerusalemu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yehova akuti: samalani kuti pa tsiku la Sabata musanyamule katundu kapena kulowa naye pa zipata za Yerusalemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
atero Yehova: Tadziyang'anirani nokha, musanyamule katundu tsiku la Sabata, musalowe naye pa zipata za Yerusalemu;