Jeremiah 17:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwowo sadamvere kapena kusamalako, koma ndi mitima yokanika adakana kumva ndi kulandira malangizo anga.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
koma sanamvere, sanatchere khutu lao, koma anaumitsa khosi lao, kuti asamve asalandire langizo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komatu iwo sanandimvere kapena kulabadira. Ndi mitima yawo yowumayo sanamvere kapena kulandira malangizo anga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
koma sanamvera, sanachera khutu lao, koma anaumitsa khosi lao, kuti asamve, asalandire langizo.