Jeremiah 17:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chuma chanu ndi katundu wanu yense ndidzazipereka kwa ofunkha, kuti zikhale dipo la machimo anu ochitika m'dziko lanu lonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwe phiri langa la m'munda, ndidzapereka chuma chako ndi zosungidwa zako zikafunkhidwe, ndi misanje yako, chifukwa cha tchimo, m'malire ako onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chuma chanu ndiponso katundu wanu yense ndidzazipereka kwa ofunkha kuti zikhale dipo lawo chifukwa cha machimo ochitika mʼdziko lonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwe phiri langa la m'munda, ndidzapereka cuma cako ndi zosungidwa zako zikafunkhidwe, ndi misanje yako, cifukwa ca cimo, m'malire ako onse.