Jeremiah 17:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mudzataya dziko limene ndidakupatsani kuti likhale ngati choloŵa chanu. Ndidzakusandutsani akapolo otumikira adani anu m'dziko limene simulidziŵa. Ndithu mkwiyo wanga uli ngati moto woyaka, ndipo udzayakadi mpaka muyaya.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Iwe, iwe wekha, udzaleka pa cholowa chako chimene ndinakupatsa iwe; ndipo ndidzakutumikiritsa adani ako m'dziko limene sulidziwa; pakuti wakoleza moto m'mkwiyo wanga umene udzatentha kunthawi zamuyaya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mudzataya dziko limene ndinakupatsani kuti likhale cholowa chanu. Ndidzakusandutsani akapolo otumikira adani anu mʼdziko limene inu simukulidziwa, chifukwa mwabutsa mkwiyo wanga ngati moto, ndipo udzayaka mpaka muyaya.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Iwe, iwe wekha, udzaleka pa colowa cako cimene ndinakupatsa iwe; ndipo ndidzakutumikiritsa adani ako m'dziko limene sulidziwa; pakuti wakoleza moto m'mkwiyo wanga umene udzatentha ku nthawi zamuyaya.