Jeremiah 17:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mtima wa munthu ndi chinthu chonyenga kwambiri kupambana zinthu zonse. Kuipa kwake nkosachizika. Kodi ndani angathe kuumvetsa?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mtima ndiwo wonyenga koposa, ndi wosachiritsika, ndani angathe kuudziwa?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mtima wa munthu ndi wonyenga kupambana zinthu zonse ndipo kuyipa kwake nʼkosachizika. Ndani angathe kuwumvetsa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mtima ndiwo wonyenga koposa, ndi wosaciritsika, ndani angathe kuudziwa?