Jeremiah 18:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Kodi chisanu chimatha pa mathanthwe otsetsereka a phiri la Lebanoni? Kodi mitsinje ya madzi ozizira ochokera ku phiri la Lebanoni imaphwa?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi matalala a Lebanoni adzalephera pa mwala wa m'munda? Kodi adzaphwa madzi ozizira otsika kutali?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi chisanu chimatha pa matanthwe otsetsereka a phiri la Lebanoni? Kodi madzi ozizira amitsinje ochokera ku phiri la Lebanoni adzamphwa?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi matalala a Lebano adzalephera pa mwala wa m'munda? kodi adzaphwa madzi ozizira otsika kutari?