Jeremiah 18:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndidzaŵabalalitsa ngati mphepo yakuvuma. Adzathaŵa pamene adani ao akufika. Ndidzaŵafulatira osaŵathandiza pa nthaŵi ya mavuto ao.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndidzamwazamwaza iwo monga ndi mphepo ya kum'mawa pamaso pa adani; ndidzayang'anira pamsana pao, si nkhope yao, tsiku la Tsoka lao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati mphepo yochokera kummawa, ndidzawabalalitsa pamaso pa adani awo; ndidzawafulatira osawathandiza pa tsiku la mavuto awo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndidzamwazamwaza iwo monga ndi mphepo ya kum'mawa pamaso pa adani; ndidzayang'anira pamsana pao, si nkhope yao, tsiku la tsoka lao.